Nsanja ya Olonda Yophunzira
APRIL 2020
NKHANI ZOPHUNZIRA: JUNE 1–JULY 5, 2020
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
M’bale J. F. Rutherford komanso abale ena odzozedwa omwe ankatsogolera gulu lathu ankalengeza molimba mtima uthenga wachiweruzo cha Mulungu kwa anthu oipa am’dzikoli (Onani nkhani yophunzira 14, ndime 8)