Magazini Yophunzira
MAY 2020
NKHANI ZOPHUNZIRA: JULY 6–AUGUST 2, 2020
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Pankhondo ya Aramagedo, Ufumu wa Mulungu umene wayerekezeredwa ndi mwala, udzathetsa maulamuliro a anthu, omwe akuimiridwa ndi chifaniziro chachikulu (Onani nkhani yophunzira 20, ndime 11)