Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w20 July tsamba 1-32
  • Nsanja Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nsanja Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
w20 July tsamba 1-32
Nsanja ya Olonda Yophunzira, July 2020.

Magazini Yophunzira

JULY 2020

NKHANI ZOPHUNZIRA: AUGUST 31–SEPTEMBER 27, 2020

© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:

Davide sanaope kumenyana ndi Goliati ngakhale kuti anali wamng’ono ndipo ankaoneka ngati wopanda mphamvu. Iye anadalira Yehova kuti amupatse mphamvu zogonjetsera Goliati ndipo anamugonjetsadi (Onani nkhani yophunzira 29, ndime 11)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena