Nsanja ya Olonda Yophunzira
AUGUST 2020
NKHANI ZOPHUNZIRA: SEPTEMBER 28–NOVEMBER 1, 2020
© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Yesu ali kumwamba, kumbuyo kwake kuli olamulira anzake omwe akuyang’ana angelo ambirimbiri. Angelo ena akupita padziko lapansi kuti akagwire ntchito imene apatsidwa. Yehova amapereka zochita kwa onse amene akusonyezedwa pachithunzichi (Onani nkhani yophunzira 32, ndime 5)