Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw Library Komanso Jw.Org
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Ali m’ndende ku Eritrea, munthu wina anadzionera yekha kuti a Mboni za Yehova amachita zimene amaphunzitsa ena pa moyo wawo.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > EXPERIENCES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > ANAKHALABE OKHULUPIRIKA ATAKUMANA NDI MAYESERO.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingatani Kuti Ndisamapanikizike Kwambiri?
Kodi n’chiyani chimayambitsa vuto la kupanikizika? Kodi inunso mumapanikizika kwambiri? Ngati ndi choncho, kodi mungatani kuti muthane ndi vutoli?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > YOUNG PEOPLE ASK.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.