Magazini Yophunzira
JUNE 2021
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: AUGUST 2-29, 2021
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
M’bale ndi mkazi wake akuphunzira Baibulo ndi wachinyamata wina ndipo akugwiritsa ntchito buku lakuti Mungakhale ndi Moyo Mpaka Kalekale (Onani nkhani yophunzira 22, ndime 2)