Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIMU MULI
Nkhani Yophunzira 26: August 30, 2021–September 5, 2021
2 Kodi Mungagwire Nawo Ntchito Yothandiza Anthu Kukhala Ophunzira a Yesu?
Nkhani Yophunzira 27: September 6-12, 2021
8 Muzitsanzira Yehova pa Nkhani ya Kupirira
Nkhani Yophunzira 28: September 13-19, 2021
14 Muzipewa Kuyambitsa Mpikisano Koma Muzilimbikitsa Mtendere
Nkhani Yophunzira 29: September 20-26, 2021
20 Muzisangalala ndi Zimene Mukuchita Potumikira Yehova
26 Mbiri ya Moyo Wanga—Ndakhala Ndikusangalala Potumikira Yehova