Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Mmene Sukulu ya Giliyadi Imathandizira Padziko Lonse
Sukulu yofunika kwambiriyi imachitikira ku New York, koma ophunzira ake amachokera m’mayiko osiyanasiyana padziko lonse. Ndiye kodi zimatani kuti ophunzirawa akafike kusukuluyi?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > HOW YOUR DONATIONS ARE USED.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti LAIBULALE> NKHANI ZOSIYANASIYANA > KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Pa nthawi ina Erwin Lamsfus anafunsa mnzake kuti, “Kodi unayamba wadzifunsapo chifukwa chake tili ndi moyo?” Yankho la funsoli linasintha moyo wake.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > THE BIBLE CHANGES LIVES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > BAIBULO LIMASINTHA ANTHU.