Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Madzi Osefukira Anabweretsa Uthenga Wabwino
Anthu a m’midzi ina ku Nicaragua komwe kunasefukira madzi analandira thandizo, pamene a Mboni za Yehova othandiza pakachitika ngozi anagwiritsa ntchito boti kukathandiza anthu komanso kuwalimbikitsa ndi uthenga wabwino.
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > EXPERIENCES OF JEHOVAH’S WITNESSES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA > KUUZA ENA CHOONADI CHA M’BAIBULO.
KALE LATHU
Anapereka Zinthu Zawo Zabwino Kwambiri
Kodi a Mboni za Yehova anathandiza bwanji Akhristu anzawo a ku Germany nkhondo yachiwiri ya padziko lonse itatha?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > FROM OUR ARCHIVES.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > KALE LATHU.