Zimene Zili M’magaziniyi
M’MAGAZINIYI MULI
Nkhani Yophunzira 6: April 4-10, 2022
2 Kodi Mumakhulupirira Kuti Yehova Amachita Zinthu M’njira Yoyenera?
Nkhani Yophunzira 7: April 11-17, 2022
Nkhani Yophunzira 8: April 18-24, 2022
14 Kodi Malangizo Amene Mumapereka ‘Amasangalatsa Mtima’?
Nkhani Yophunzira 9: April 25, 2022–May 1, 2022
20 Muzitsanzira Yesu Potumikira Ena
26 Mbiri ya wanga Moyo—Ndinapeza Chinthu Choposa Ntchito ya Udokotala
30 Kodi Mukudziwa?—N’chifukwa chiyani Aisiraeli ankapereka malowolo?