Magazini Yophunzira
MARCH 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: MAY 2–JUNE 5, 2022
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Zekariya anaona masomphenya a mitengo iwiri ya maolivi, yomwe inkathira mafuta muchoikapo nyale chomwe chinali ndi nyale 7 (Onani nkhani yophunzira 12, ndime 6)