Magazini Yophunzira
MAY 2022
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JULY 4–AUGUST 7, 2022
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Pa Chivumbulutso 21 amafotokoza za mzinda wophiphiritsa wa Yerusalemu Watsopano “ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu.” Mu ulamuliro wa zaka 1000, mzindawu udzabweretsa madalitso ochuluka kwa anthu omvera (Onani nkhani yophunzira 21, ndime 14-16)