Nkhani Zimene Zatuluka Pa JW Library Komanso JW.ORG
NKHANI ZINA
Kodi Zipembedzo Ziyenera Kuchita Nawo Zandale?
Padziko lonse, anthu omwe amati ndi otsatira a Yesu Khristu amalowerera kwambiri munkhani zandale. Kodi ayeneradi kumachita zimenezi?
ZOCHITIKA PA MOYO WA A MBONI ZA YEHOVA
Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Albania ndi ku Kosovo
Kodi omwe anakalalikira kumene kunkafunika ofalitsa ambiriwa anapeza chimwemwe chotani, chomwe chinawathandiza kupirira ngakhale kuti ankakumana ndi mavuto?
KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?
Nyimbo Zomwe Zimatithandiza Kuyandikira Mulungu
Pa nyimbo zathu za broadcasting, kodi pali yomwe mumaikonda kwambiri? Kodi munayamba mwaganizirapo mmene inakonzedwera?