Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w23 December tsamba 1-32
  • Magazini Yophunzira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Magazini Yophunzira
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
w23 December tsamba 1-32
Mkhristu wachinyamata ndi wachitsikana akukula mwauzimu ndipo akusangalala. Mlongoyo watenga Baibulo ndipo akuganizira mozama pomwe m’baleyo akulalikira. Zithunzi: Akhristu achinyamata ndi achitsikana akuchita zinthu zokhudza kulambira. 1. Mlongo akuika zinthu patebulo ku Beteli. 2. Alongo awiri akuwerengera munthu Baibulo mu utumiki. 3. Mlongo akulalikira ndi mlongo wachikulire pogwiritsa ntchito kashelefu. 4. M’bale akuthandiza m’bale wachikulire kuti aone zinthu zina patabuleti yake. 5. M’bale akuwerenga Baibulo kupulatifomu pamisonkhano ya mpingo. 6. M’bale akugwiritsa ntchito mashini ochekera matabwa pa ntchito ya zomangamanga.

Magazini Yophunzira

DECEMBER 2023

NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: FEBRUARY 5–MARCH 3, 2024

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:

Alongo ndi abale ambiri achinyamata amene anaphunzitsidwa mfundo za m’Malemba n’kumazitsatira amakula mwauzimu (Onani nkhani yophunzira 52 ndime 21, ndi nkhani yophunzira 53, ndime 19-20)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena