Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova 2013
Muli Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2012
Buku lino ndi la ․․․․․
© 2013
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA.
Ofalitsa
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF SOUTH AFRICA NPC. 1 Robert Broom Drive East, Rangeview, Krugersdorp, 1739, R.S.A.
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsa anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
M’bale wa m’Komiti ya ku Yangon Yopereka Chithandizo Pakagwa Tsoka akukonza zinthu zimene zinawonongedwa ndi mphepo yamkuntho ya Nargis (tsamba 163)