Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yb15 tsamba 8-tsamba 9 ndime 1
  • Zimene Zachitika M’chaka Chapitachi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Zachitika M’chaka Chapitachi
  • Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015
  • Nkhani Yofanana
  • Ulemerero wa Yehova Umawalira Anthu Ake
    Nsanja ya Olonda—2002
  • “M’mapiri Ake Mudzakumbamo Mkuwa”
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Baibulo Lomveka Bwino Kwambiri
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Kuyenda M’njira ya Kuunika Komawalabe
    Nsanja ya Olonda—2006
Onani Zambiri
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015
yb15 tsamba 8-tsamba 9 ndime 1
Chithunzi pamasamba 8, 9

Zimene Zachitika M’chaka Chapitachi

Yehova Mulungu anauzira mneneri Yesaya kulosera kuti: “M’malo mwa mkuwa, ndidzabweretsa golide. M’malo mwa chitsulo, ndidzabweretsa siliva. M’malo mwa mtengo, ndidzabweretsa mkuwa ndipo m’malo mwa miyala, ndidzabweretsa chitsulo.” (Yes. 60:17) Lembali likusonyeza kuti zinthu wamba zikulowedwa m’malo ndi zinthu zamtengo wapatali. Izi zikuimira kupita patsogolo kwa gulu la Yehova. M’chaka chapitachi ulosiwu wakwaniritsidwa m’njira zambiri. Kunena zoona zinthu zakhala zikutiyendera bwino kwambiri m’nthawi yamapeto ino.—Mat. 24:3.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena