Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ijwcl nkhani 26
  • Anapeza “Ngale . . . Yamtengo Wapatali”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anapeza “Ngale . . . Yamtengo Wapatali”
  • Baibulo Limasintha Anthu
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Kupeza Ngale Imodzi ya Mtengo Wapatali’
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Kufunafuna ‘Ngale ya Mtengo Wapatali’ Lerolino
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Tizikonda ndi Mtima Wonse Chuma Chimene Mulungu Watipatsa
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Kudalitsidwa ndi Malangizo Owonjezereka
    Nsanja ya Olonda—1987
Onani Zambiri
Baibulo Limasintha Anthu
ijwcl nkhani 26

BAIBULO LIMASINTHA ANTHU

Anapeza “Ngale . . . Yamtengo Wapatali”

Yesu anaphunzitsa kuti Ufumu wa Mulungu udzathetsa mavuto onse omwe anthu akukumana nawo. (Mateyu 6:10) Pa Mateyu 13:44-46, iye anafotokoza mafanizo awiri otsatirawa pofuna kusonyeza kufunika kwa choonadi chonena za Ufumu wa Mulungu:

Zithunzi: Amuna awiri omwe anatchulidwa mufanizo la Yesu. 1. Munthu akulima m’munda ndipo akudabwa ndi zomwe waona. 2. Munthu wina ali ndi ngale m’manja ndipo akumwetulira.
  • Mwamuna wina ankalima m’munda, kenako mwadzidzidzi anaona chuma chomwe chinabisidwa m’mundamo.

  • Munthu wina wochita malonda amene ankayendayenda pofufuza ngale zabwino, anapeza ngale imodzi yamtengo wapatali.

Anthu awiriwa, anagulitsa katundu wawo yense kuti apeze zinthu zamtengo zomwe anaona. Amunawa akuimira anthu omwe amaona zinthu zokhudza Ufumu kukhala zofunika kwambiri moti amalolera kusintha zinthu zambiri pa moyo wawo ndi cholinga choti apeze madalitso a Ufumuwo. (Luka 18:29, 30) Muvidiyoyi muphunzira za anthu awiri omwe anachita zinthu ngati amuna otchulidwa mufanizo la Yesu.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena