1 MAFUMU
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Davide ndi Abisagi (1-4)
Adoniya ankafuna kukhala mfumu (5-10)
Zimene anachita Natani ndi Bati-seba (11-27)
Davide analamula kuti Solomo adzozedwe kukhala mfumu (28-40)
Adoniya anathawira kuguwa la nsembe (41-53)
2
Davide analangiza Solomo (1-9)
Davide anamwalira; Solomo anakhala mfumu (10-12)
Zimene Adoniya anachita zinamuphetsa (13-25)
Abiyatara anathamangitsidwa; Yowabu anaphedwa (26-35)
Simeyi anaphedwa (36-46)
3
Solomo anakwatira mwana wa Farao (1-3)
Yehova anaonekera kwa Solomo mʼmaloto (4-15)
Solomo anaweruza azimayi awiri (16-28)
4
Ulamuliro wa Solomo (1-19)
Zinthu zinkayenda bwino mu ulamuliro wa Solomo (20-28)
Nzeru za Solomo ndi miyambi yake (29-34)
5
6
7
Nyumba yachifumu ya Solomo (1-12)
Hiramu waluso anathandiza Solomo (13-47)
Zipilala ziwiri zakopa (15-22)
Thanki yosungira madzi (23-26)
Zotengera 10 zakopa (27-39)
Anamaliza kupanga zinthu zagolide (48-51)
8
Anabweretsa Likasa mʼkachisi (1-13)
Solomo analankhula ndi anthu (14-21)
Pemphero la Solomo lotsegulira kachisi (22-53)
Solomo anadalitsa anthu (54-61)
Nsembe ndi chikondwerero chotsegulira kachisi (62-66)
9
Yehova anaonekeranso kwa Solomo (1-9)
Mphatso zimene Solomo anapatsa Hiramu (10-14)
Zinthu zimene Solomo anamanga (15-28)
10
11
Akazi a Solomo anapotoza mtima wake (1-13)
Anthu amene ankalimbana ndi Solomo (14-25)
Yerobowamu analonjezedwa mafuko (26-40)
Solomo anamwalira; Rehobowamu anakhala mfumu (41-43)
12
Rehobowamu sanayankhe bwino anthu (1-15)
Mafuko 10 anagalukira Solomo (16-19)
Yerobowamu anakhala mfumu ya Isiraeli (20)
Rehobowamu anamuletsa kuti asakamenyane ndi Aisiraeli (21-24)
Yerobowamu anayamba kulambira mwana wa ngʼombe (25-33)
13
14
15
Abiyamu, mfumu ya Yuda (1-8)
Asa, mfumu ya Yuda (9-24)
Nadabu, mfumu ya Isiraeli (25-32)
Basa, mfumu ya Isiraeli (33, 34)
16
Yehova anaweruza Basa (1-7)
Ela, mfumu ya Isiraeli (8-14)
Zimiri, mfumu ya Isiraeli (15-20)
Omuri, mfumu ya Isiraeli (21-28)
Ahabu, mfumu ya Isiraeli (29-33)
Hiyeli anamanganso Yeriko (34)
17
Mneneri Eliya analosera chilala (1)
Akhwangwala ankabweretsera Eliya chakudya (2-7)
Eliya anapita kwa mkazi wamasiye wa ku Zarefati (8-16)
Mwana wa mkazi wamasiye anamwalira nʼkuukitsidwa (17-24)
18
Eliya anakumana ndi Obadiya ndi Ahabu (1-18)
Eliya ndi aneneri a Baala paphiri la Karimeli (19-40)
Chilala cha zaka zitatu ndi hafu chinatha (41-46)
19
Eliya anathawa Yezebeli (1-8)
Yehova anaonekera kwa Eliya ku Horebe (9-14)
Eliya anadzoza Hazaeli, Yehu ndi Elisa (15-18)
Elisa anadzozedwa kuti alowe mʼmalo mwa Eliya (19-21)
20
Asiriya anamenyana ndi Ahabu (1-12)
Ahabu anagonjetsa Asiriya (13-34)
Ulosi wotsutsana ndi Ahabu (35-43)
21
Ahabu anasirira munda wa Naboti (1-4)
Yezebeli anakonza zoti Naboti aphedwe (5-16)
Uthenga wa Eliya wotsutsa Ahabu (17-26)
Ahabu anadzichepetsa (27-29)
22
Yehosafati anachita mgwirizano ndi Ahabu (1-12)
Mikaya analosera kuti Ahabu agonjetsedwa (13-28)
Ahabu anaphedwa ku Ramoti-giliyadi (29-40)
Yehosafati anakhala mfumu ya Yuda (41-50)
Ahaziya mfumu ya Isiraeli (51-53)