YONA
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Yona ankafuna kuthawa Yehova (1-3)
Yehova anayambitsa chimphepo (4-6)
Mavuto anayamba chifukwa cha Yona (7-13)
Yona anaponyedwa mʼnyanja (14-16)
Chinsomba chinameza Yona (17)
2
3
Yona anamvera Mulungu nʼkupita ku Nineve (1-4)
Anthu a ku Nineve analapa atamva uthenga wa Yona (5-9)
Mulungu anaganiza zoti asawononge Nineve (10)
4