NAHUMU ZIMENE ZILI MʼBUKULI 1 Mulungu analanga adani ake (1-7) Mulungu amafuna kuti tizidzipereka kwa iye yekha (2) Yehova amadziwa anthu amene amathawira kwa iye (7) Nineve adzawonongedwa (8-14) Mavuto sadzachitikanso (9) Uthenga wabwino wokhudza Yuda unalengezedwa (15) 2 Nineve adzakhala bwinja (1-13) “Zotsekera madzi amʼmitsinje zidzatsegulidwa” (6) 3 “Tsoka mzinda wokhetsa magazi” (1-19) Zomwe zidzachititse kuti Nineve awonongedwe (1-7) Nineve adzawonongedwa ngati No-amoni (8-12) Nineve sadzalephera kuwonongedwa (13-19)