2 AKORINTO
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
Paulo ankafuna kuti Akhristu a ku Korinto asangalale (1-4)
Wochimwa anakhululukidwa nʼkubwezeretsedwa (5-11)
Paulo anapita ku Torowa ndiponso ku Makedoniya (12, 13)
Utumiki, kuguba ponyadira kupambana (14-17)
3
Makalata otichitira umboni (1-3)
Atumiki a pangano latsopano (4-6)
Ulemerero wa pangano latsopano ndi waukulu (7-18)
4
5
6
Osagwiritsa ntchito molakwa kukoma mtima kwa Mulungu (1, 2)
Utumiki wa Paulo (3-13)
Musamangidwe mʼgoli ndi osakhulupirira (14-18)
7
Tidziyeretse kuchotsa choipitsa chilichonse (1)
Paulo anasangalala ndi Akorinto (2-4)
Tito anabwera ndi lipoti labwino (5-7)
Chisoni chogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndiponso kulapa (8-16)
8
9
10
11
12
Masomphenya a Paulo (1-7a)
“Minga mʼthupi” la Paulo (7b-10)
Sankachepa poyerekezera ndi atumwi apamwamba (11-13)
Paulo ankadera nkhawa Akorinto (14-21)
13