Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g00 3/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2000
  • Nkhani Yofanana
  • Ukapolo Ndi Khalidwe Lankhanza Lomwe Lidakalipobe
    Galamukani!—2002
  • Akapolo Anapeza Ufulu M’mbuyomu Komanso Masiku Ano
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2017
  • Kodi Ndani Ali Akapolo Lerolino?
    Galamukani!—2000
  • Kodi Mulungu Ankakondwera ndi Malonda a Ukapolo?
    Galamukani!—2001
Onani Zambiri
Galamukani!—2000
g00 3/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

March 8, 2000

Ukapolo Wamakono—Uli Pafupi Kutha!

Anthu miyandamiyanda, makamaka amayi ndi ana, akukhala monga akapolo enieni. Kodi ukapolo umenewu udzatha bwanji?

3 Chinsinsi Chosaululidwa

5 Kodi Ndani Ali Akapolo Lerolino?

9 Ukapolo Wamakono Uli Pafupi Kutha!

13 Kudzipha—Mliri Wobisika

15 Tinapatsidwa Chikhumbo Chokhala ndi Moyo

18 Chiyembekezo Chotsimikizika

20 Lingaliro la Baibulo

Kodi Chikhulupiriro Choona N’chiyani?

32 “Ndiyenera Kudalira Mulungu”

Anthu a ku Russia Akuyamikira Ufulu wa Kulambira 22

Kuyambira mu 1991, anthu okhala m’dziko lomwe kale linkatchedwa Soviet Union akhala ndi ufulu waukulupo wa kulambira Mulungu. Anthu amene anachoka m’dzikolo kukakhala m’mayiko ena ayamikiranso ufulu wotere.

N’chifukwa Chiyani Bwenzi Langa Linandikhumudwitsa? 29

Nthaŵi zina ubwenzi umasokonezeka. Kodi zimenezi zimachitika bwanji? Kodi mungachitepo Chiyani Pankhaniyi?

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

CHIKUTO: Kuzungulira kuyambira pamwamba chakumanja: CHITHUNZI CHA UN 148000/Jean Pierre Laffont; UNITED NATIONS/ J.P. LAFFONT; J.R. Ripper/RF2; J.R. Ripper/RF2; CHITHUNZI CHA UN 152227 chojambulidwa ndi John Isaac; pakati: Chithunzi cha United Nations: 151730

UNITED NATIONS/J.P. LAFFONT

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena