Zamkatimu
June 8, 2000
Zithunzi Zamaliseche za pa Intaneti—Kodi Zingavulaze Motani?
Kodi kuona zithunzi zamaliseche pa intaneti kuli n’zoopsa zanji? Kodi zimenezi n’kuzipeŵa motani?
3 Zithunzi Zamaliseche Zayamba Kupezeka pa Intaneti
7 Dzitetezeni Nokha Ndiponso Okondedwa Anu
11 Pamene Nthenda Yaikulu Yagwira Banja
12 Matenda Aakulu Ndi Nkhani ya Banja Lonse
16 Mmene Mabanja Amapiririra Matenda Aakulu
26 Anthu Amakono Okhala M’mapanga
28 Mmene Banja Lathu Linagwirizanirananso
Kodi Abambo Angathaŵedi Ana Awo? 21
Kodi mnyamata angathaŵedi mavuto obwera chifukwa chokhala ndi mwana asanakwatire?
Kodi Baibulo limayankha bwanji funso limeneli?