Zamkatimu
September 8, 2000
Kuona Zimene Maso Anu Sangathe Kuona
Pali zinthu zambiri zimene maso paokha sangaone. Kodi n’chiyani chimene chimaonekera poyang’anitsitsa zinthu zimene maso a munthu satha kuona paokha? Kodi zingakhudze bwanji moyo wanu?
3 Zimene Diso Palokha Silingaone
5 Kodi Kuyang’anitsitsa Zinthu Zosaoneka Kumavumbula Chiyani?
10 Kodi Mumaona Zina Zimene Maso Anu Saona?
12 Khama Langa Lofuna Kusankha Zinthu Mwanzeru
19 Kuchoka ku Olympia Kukachitira ku Sydney
20 Zolinga za Olimpiki Zakanika
26 Chivomezi!
31 Kuthandiza Achinyamata Kusiya Kupulupudza
32 Kodi Anthu Adzasiya Mkhalidwe Wauchinyama?
Kodi Ndingachitenji Ndikamavutitsidwa ndi Amuna Kapena Akazi? 16
Kodi wachinyamata wachikristu angathane nalo bwanji khalidwe loipa limeneli? Kodi pali njira iliyonse yolipeŵera?
[Chithunzi patsamba 2]
Asayansi akufufuza tinthu tina topanga magawo a ma atomu