Zamkatimu
October 8, 2001
Kodi Tingadzale Chakudya Chokwanira?
Kutakhala kopanda mbewu zodyedwa anthu angathe kufa ndi njala. Sayansi yathandiza kwambiri kuchulukitsa mbewu zofunikazi. Koma kodi potero yadzetsa mavuto ena ochuluka?
3 Kodi Anthu Akudziwonongera Okha Chakudya?
4 Mitundu Yosiyanasiyana ya Zinthu N’njofunika M’moyo
9 Kodi Adzadyetse Dziko Ndani?
18 Kodi Zikondwerero Zotchuka Zilibe Vuto Lililonse?
19 Zoona Zake za Zikondwerero Zotchuka
25 Mzinda wa mu Africa Umene uli ndi Anthu a Chikhalidwe Chosiyanasiyana
19 Nkhuku Zimakondedwa ndi Anthu Ambiri Ndiponso N’zochuluka
Kodi Ndingatani Kuti Ndisamade Nkhaŵa Kwambiri? 12
Nkhaŵa zingakuchititseni kuti mukhale munthu wodandaula kwambiri. Kodi vuto la nkhaŵali mungalimbane nalo bwanji?
Kodi Mulungu N’ngolekerera Motani? 28
Kodi tingati n’chifukwa chiyani Mulungu walekerera zoipa?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
CHIKUTO: Mayi ali m’munda: Godo-Foto; tsamba 2 chithunzi chachikulu: U.S. Department of Agriculture