Zamkatimu
April 8, 2002
Kodi Kukhala Mayi N’kolira Ukatswiri?
Kodi masiku ano mavuto ena a kukhala mayi ndi otani? Kodi n’kuwatha motani?
3 Amayi Amachita Ntchito Zambiri
4 Kukhala Mayi N’chintchito Chovuta
8 Kulimbana ndi Mavuto Okhala Mayi
17 Kuthandiza Anthu Amene Ataya Mtima Pakati pa Zoopsa
18 Mmene Chivomezi Chimachitikira
20 Kuthana ndi Mavuto Obwera ndi Chivomezi
23 Mmene Zivomezi ndi Maulosi a Baibulo Zimakukhudzirani
Kodi Akristu Ayenera Kuganiza Kuti Mulungu Azingowateteza? 12
Kodi Baibulo limati chiyani pankhani imeneyi?
Chinenero cha Kutchire—Kulankhulana Kodabwitsa kwa Zinyama 24
Kodi zinyama ‘zimalankhulana’ bwanji?