Zamkatimu
August 8, 2003
Kodi Chikuchitika N’chiyani ndi Nyengoyi?
M’madera ambiri padziko lonse, kusintha kodabwitsa kwa nyengo kwawonongetsa zinthu zambiri. Kodi zimenezi zikusonyeza kuti nyengo yasokonekera
5 Kodi Chikuchitika N’chiyani ndi Nyengoyi?
8 Sikudzakhalanso Masoka Chifukwa cha Nyengo!
10 Chimene Mkuntho Sunathe Kukokolola
19 Anthu Akusiyana Maganizo pa Zithunzi Zolaula
20 N’chifukwa Chiyani Zithunzi Zolaula Zatenga Malo?
22 Zithunzi Zolaula N’zowononga
27Achinyamata Akufunsa Kuti . . .
N’chifukwa Chiyani Ndimafuna Kumangochita Chilichonse Mosalakwitsa?
32 Kalata Yochokera kwa Wokondedwa
Kodi Kudana ndi Anthu Amitundu Ina N’koyenera? 30
Kudana ndi anthu a mitundu ina kwaphetsa anthu ambiri, ngakhale m’zaka za posachedwapa. Kodi Baibulo limavomereza zimenezi m’njira ina iliyonse?