Zamkatimu
October 8, 2003
Ulimi N’chifukwa Chiyani Sukuyenda Bwino?
M’mayiko ambiri alimi tsopano akukumana ndi mavuto osaneneka a zachuma. Kodi chikuchititsa mavuto a zaulimi n’chiyani, nanga angathetsedwe bwanji?
3 Mavuto Amene Alimi Amakumana Nawo
5 Kodi Chikuchititsa Mavuto A Zaulimi N’chiyani?
12 Zitaphulika
19 Kulankhulana N’kofunika Kwambiri Pakati pa Zachilengedwe za Padziko Lapansi
20 Kulankhulana kwa Zachilengedwe
26 Kulankhulana Kumene Kumapatsa Moyo
Kodi Ndilembe Chizindikiro pa Thupi Langa? 16
N’chifukwa chiyani achinyamata ambiri amatengeka ndi zizindikiro za pa thupi? Kodi pali mfundo zotani zofunika kuziganizira?
Njira Zisanu ndi Imodzi Zosamalira Thanzi Lanu 27
Matenda ambiri angapeŵedwe potsatira njira zosavuta izi.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Mark Segal/Index Stock Photography