Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g04 6/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2004
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mungatani Ngati Mumasowa Wocheza Naye?
    Galamukani!—2015
  • Nthaŵi Imene Sipadzakhalanso Munthu Wosungulumwa
    Galamukani!—2004
  • N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Ali Osungulumwa?
    Galamukani!—2004
  • N’chifukwa Chiyani Ndilibe Anzanga Enieni?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
Onani Zambiri
Galamukani!—2004
g04 6/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

June 8, 2004

Kukhala Nokhanokha Koma Osasungulumwa

N’chifukwa chiyani anthu ambiri ali osungulumwa? Kodi munthu angachite chiyani kuti athane ndi kusungulumwa? Kodi padzakhala nthaŵi imene sipadzakhalanso munthu wosungulumwa?

3 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Ali Osungulumwa?

5 Kuthana ndi Kusungulumwa

9 Nthaŵi Imene Sipadzakhalanso Munthu Wosungulumwa

18 N’chifukwa Chiyani Anthu Ambiri Amadwala Chimfine Chimene Chimabwera Akakhala Pafupi ndi Mungu?

19 Nkhondo Yakalekale Yofuna Kupeza Thanzi Labwino

23 Kupambana ndi Kulephera pa Nkhondo Yolimbana ndi Matenda

27 Dziko Lopanda Matenda

30 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .

N’chifukwa Chiyani Chibwenzi Changa Chimandizunza Chonchi?

Matayala Angapulumutse Moyo Wanu 12

Matayala abwino ndi ofunika kwambiri kuti galimoto isachite ngozi. Kodi mungawasamale bwanji?

Kodi Kuda Nkhaŵa N’kupanda Chikhulupiriro? 16

Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani imeneyi?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena