Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g04 12/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2004
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Kupeza Chibwenzi pa Intaneti Kungakhaledi Koopsa?
    Galamukani!—2005
  • Muzisankha Mwanzeru Anthu Ocheza Nawo
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Tiyenera Kugwiritsa Ntchito Intaneti Mwanzeru
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Kodi Tingapeze Bwanji Anzathu Abwino?
    Nsanja ya Olonda—2011
Onani Zambiri
Galamukani!—2004
g04 12/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

December 8, 2004

Kodi Edzi Idzatha Liti?

Kwa zaka pafupifupi 20, madokotala ndi ochita kafukufuku wa zamankhwala padziko lonse lapansi akhala akugwira ntchito mwakhama polimbana ndi Edzi. Kodi panopa tatsala pang’ono kuthetsa nthenda yoopsa imeneyi?

3 Mankhwala a Edzi Akufunika Kwambiri!

5 Zinthu Zolimbikitsa Zimene Zachitika pa Ntchito Yolimbana ndi Edzi

10 Kodi Edzi Idzatha Liti?

12 Zimene Mungachite Munthu Amene Mumakonda Akadwala Misala

15 “Aliyense Ayenera Kuwerenga Buku Limeneli”

16 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Kusudzulana N’kuthetsadi Mavuto?

19 Tonsefe Timafunika Kukhala ndi Anzathu

20 Kupeza Anzathu Omwe Timalakalaka

24 Pali Anzanu Abwino ndi Anzanu Oipa

32 Mlozera Nkhani wa Voliyumu 85 ya Galamukani!

Khoti la ku Ulaya Linalemekeza Ufulu wa Mayi 18

Khoti lina lalikulu linakonzanso zinthu kuti zikhale bwino mayi wina ndi ana ake atachitiridwa zinthu zopanda chilungamo kwambiri.

Kodi Ndingachite Chiyani Ndikalephera? 29

Achinyamata ambiri amaopa kulephera. Komabe, aliyense amalakwitsa zinthu nthawi zina. Kodi mungatani kuti mupewe kupwetekedwa mtima mukalephera?

[Chithunzi pachikuto]

PACHIKUTO: KU UNITED STATES Wodwala Edzi akufuna kumwa mitundu 14 ya mankhwala osiyanasiyana amene amamwa katatu tsiku lililonse

[Mawu a Chithunzi]

COVER: Photo by Joe Raedle/Getty Images

[Chithunzi patsamba 2]

KU SOUTH AFRICA Ana awiri akungodikira kuti makolo awo amwalire ndi Edzi

[Mawu a Chithunzi]

© Paul Weinberg/Panos Pictures

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena