Zamkatimu
February 2007
Kodi Zipembedzo Zikutha Mphamvu?
Tikamamva zakuti m’mayiko ena anthu ayamba kuchepa kwambiri m’matchalitchi achikhristu pamene m’mayiko ena ayamba kuchuluka, zimavuta kumvetsa kuti chikuchitika n’chiyani makamaka. Kodi tsogolo la matchalitchi n’lotani?
3 Kodi Matchalitchi Akulowera Kuti?
4 Kodi N’chiyani Chikuchitika M’matchalitchi?
7 Kodi Chikhristu Chili ndi Tsogolo Lotani?
10 Misondodzi Ilipo Yosiyasiyana
14 Kukhala Pafupi ndi Chimphona Chimene Chili M’tulo
18 Nkhwali Yachilendo ku Hawaii
20 Bwanji Zolumbira Kukhala Odzisunga?
21 Mmene Mungachitire ndi Mavuto a Kuchuluka kwa Magalimoto Pamsewu
24 Svalbard Dera Lozizira la M’mphepete mwa Nyanja
28 Zimene Achinyamata Amadzifunsa
Kodi Ndingapewe Bwanji Khalidwe Lofuna Kugonana ndi Amuna Kapena Akazi Anzanga?
32 Ukwati Wawo Unapulumutsidwa