Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 7/07 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2007
  • Nkhani Yofanana
  • Gombe Lochititsa Chidwi la Shark Bay
    Galamukani!—2007
  • Kodi Muli ndi Vuto Losiyanitsa Mitundu?
    Galamukani!—2007
  • Khungu la Shaki
    Kodi Zinangochitika Zokha?
  • Nsomba za Shaki Zikutha
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 7/07 tsamba 1-2

Zamkatimu

July 2007

Mbalame Zimatsogoleredwa ndi Nzeru Zachibadwa Nanga Bwanji Anthu?

Anthu ambiri amangokhala osadziwa kuti chabwino ndi chiti kapena choipa ndi chiti. Komanso sadziwa kumene moyo wawo ukulowera. Werengani nkhaniyi kuti mumve malangizo abwino okutsogolerani pamoyo, komanso kuti mukhale ndi chiyembekezo cha moyo wabwino.

3 Mbalame Zili ndi Nzeru Zachibadwa Zodabwitsa

4 Kutsogoleredwa ndi Nzeru Zapamwamba Kuposa Zachibadwa

8 Muloleni Mulungu Akutsogolereni ku “Moyo Weniweni”

13 Kodi Ndani Ali ndi Pensulo?

18 Kodi Muli ndi Vuto Losiyanitsa Mitundu?

20 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Timangofunikira Kukhala Wabwino?

22 Zochitika Padzikoli

23 Nthenga Zinapangidwa Modabwitsa

26 “Yehova, Ndiloleni Kuti Ndikutumikireni”

30 Kodi Anakhaladi ndi Moyo Wautali Choncho?

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 “Izitu N’zimene Timafunikira!”

N’chifukwa Chiyani Ndimasowa Anthu Ocheza Nawo? 10

Kodi mumasungulumwa ngati anthu safuna kuchita nanu zinthu? Werengani nkhaniyi kuti mumve mmene Baibulo lingakulimbikitsireni ndi kukuthandizani.

Gombe Lochititsa Chidwi la Shark Bay 15

Werengani za malo ochititsa chidwi otetezerako zinthu zachilengedwe kumene anthu amachita kudyetsa anamgumi otchedwa dolphin ndi manja m’nyanja.

[Mawu a Chithunzi patsamba 2]

© GBRMPA

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena