Zamkatimu
June 2008
Kodi Ana Anu Mumawadziwa Bwino?
Ana ambiri amasintha makhalidwe ndiponso maonekedwe awo mwamsanga. Kodi makolo angawathandize bwanji pa nkhani imeneyi? Nanga kodi Baibulo lingathandize bwanji?
3 “Kodi Mwana Wangayu Watani?”
4 Polera Ana Luntha N’lofunika
12 Kumene Ndinamvera Dzina Loti Yehova
16 Kodi Akambuku Akuluakulu a ku Siberia Satheratu?
21 Kodi Magazi Akayezedwa Ndiye Kuti Alibedi Kachilombo ka HIV?
32 Msonkhano wa Chigawo wa Mboni za Yehova Wakuti “Mzimu wa Mulungu Umatitsogolera”
Kodi Ndi Bwino Kumenyana ndi Wachiwembu? 10
Kodi munthu angatani ngati wakumana ndi wachiwembu? Kodi njira yabwino yodzitetezera ndi iti?
Zidole Zina si Zongoseweretsa 26
Atsikana ambiri ali ndi zidole zoseweretsa. Werengani nkhaniyi kuti mumve mbiri ya zidole komanso kuti muone kufunika kosamala nazo.