Zamkatimu
February 2009
Dzikol—Linapangidwa Kuti Likhale ndi Zamoyo
Chilichonse chokhudza dzikoli chimasonyeza kuti linapangidwa kuti likhale ndi zamoyo. Kodi zimenezi zinangochitika zokha, kapena zikusonyeza kuti pali winawake amene anachita kuzilenga ndi cholinga? Kodi sayansi ndi Baibulo zimatiuza chiyani pankhaniyi?
3 Dzikoli Lili ndi Zamoyo Zochuluka
4 Dziko Lili pa Malo Abwino Kwambiri Mumlengalenga
6 Mphamvu Zimene Zimateteza Dziko
8 Kayendedwe ka Mpweya ndi Zinthu Zina
8 Kupereka Chinthu Chofunika Kwambiri kwa Anthu
10 Mbalame Zimawomba Makoma Mwangozi
25 “Kalankhulidwe” Kogometsa Koimba Likhweru
26 N’zotheka Ndithu Kuchepetsa Vuto la Kuiwala
32 Mmene Mungakhalire Bwenzi la Mulungu
Kodi Ndingatani Kuti Ndimuiwale? 18
Wina akathetsa chibwenzi, mnzakeyo amatha kusokonezeka maganizo kwabasi. Onani zimene mungachite ngati zimenezi zitakuchitikirani.
Sindinabwerere M’mbuyo Ngakhale Kuti Ndili ndi Matenda Olepheretsa Kuwerenga 21
Werengani nkhani yolimbikitsa ya munthu wina wa ku Denmark amene sanalole kuti matenda olepheretsa kuwerenga am’bweze m’mbuyo pa zolinga zake.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
COVER: Earth: NASA/The Visible Earth (http://visibleearth.nasa.gov/); Sun: SOHO (ESA & NASA)