Zamkatimu
May 2009
Mungatani Kuti Banja Lanu Lizigwiritsa Ntchito Mankhwala Moyenera?
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mungathandizire banja lanu kuti lisamagwiritse ntchito mankhwala a kuchipatala molakwika, zimene zingachititse kuti moyo wa banja lanu ukhale pangozi.
3 Anthu Akumwa Mankhwala Mwachisawawa
4 Kugwiritsa Ntchito Mankhwala Koyenera ndi Kosayenera
8 Njira Yabwino Yothetsera Vuto Logwiritsa Ntchito Mankhwala Mwachisawawa
11 Umboni Wosonyeza Kuti Nkhani za M’Baibulo N’zoona
15 Njovu Zikuluzikulu Zinkapezeka Paliponse ku Ulaya
25 Ziwombankhanga Zikuluzikulu Zogwira Nyama M’nkhalango
26 Kodi Mungadziwe Bwanji Kuti Muli ndi Matenda a Chithokomiro?
32 “Kodi Mungatani Kuti Mudzapulumuke Mapeto a Dzikoli?”
Kodi Mulungu Amafuna Kuti Mukhale Wolemera? 12
Abusa ena otchuka amanena kuti Mulungu amafuna kuti tikhale olemera. Koma kodi inoyo ndi nthawi yoyenera yofunafuna chuma? Kapena kodi pali zinthu zina zofunika kwambiri kuposa chuma?
Ndinathawa Nkhondo Ndipo Ndinapeza Moyo 21
Werengani nkhani yochititsa chidwi ya mnyamata wina amene anathawa ku Cambodia panthawi ya ulamuliro wankhanza.