Zamkatimu
September 2009
Achinyamata—Kodi Mungathane Bwanji Ndi Mavuto Anu?
Kodi mukuganiza kuti achinyamata a masiku ano akukumana ndi mavuto ambiri kuposa amene achinyamata ankakumana nawo kale? Ngati mukuganiza kuti akukumana ndi ambiri, kodi mavuto ake ndi otani? Kodi mfundo za m’Baibulo zingathandize bwanji achinyamata kuthana ndi mavuto amenewa?
3 Kodi Achinyamata Amakumana ndi Mavuto Otani?
7 Kodi Achinyamata Angapeze Bwanji Thandizo?
12 Ndakhala Wokhulupirika kwa Mulungu kwa Zaka Zoposa 70
20 Kugwiritsitsa Dzanja Lamanja la Mulungu
21 Ulimi Wamakono Wasintha Dziko
Kodi Anthu Oipa Adzakapsa Kumoto? 10
Kodi Baibulo limati chiyani pankhani imeneyi? Ndipo n’chifukwa chiyani muyenera kudziwa zolondola zokhudza nkhaniyi?
Herode Anali Katswiri pa Zomangamanga 24
Kodi Herode anamanga chiyani, ndipo n’chifukwa chiyani ophunzira a Yesu anagoma ndi zomanga zake? Kodi posachedwapa akatswiri apeza zotani zokhudza manda a Herode?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Photo: www.comstock.com