Zamkatimu
November 2009
Kodi Zipangizo Zamakono N’zothandizadi?
Mafoni am’manja, makompyuta, Intaneti ndi TV n’zofala kwambiri masiku ano. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mungagwiritsire ntchito zinthuzi mwanzeru.
3 Zipangizo Zamakono Zikuchuluka Masiku Ano
4 Kodi Zipangizo Zamakono N’zothandizadi?
6 Makolo—Muziyang’anira Ana Anu
8 Muzigwiritsa Ntchito Zipangizo Zamakono Mwanzeru
15 “Dera Loiwalika” la ku Bolivia
24 Dzina la Mulungu ku Denmark
26 Mayi Wathanzi Amaberekanso Mwana Wathanzi
32 Zimene Mukufuna Zili M’Baibulo
Kodi N’zotheka Kukonda Adani Athu? 10
Anthu akakhala ankhanza komanso achiwawa, amachititsa anthu ena kukhalanso ankhanza ndi achiwawa. Onani mmene chikondi chingathandizire kuti zimenezi zisamachitike.
Ndinasiya Usilikali N’kuyamba Kutumikira Yehova 12
Atasankhidwa kukhala mkulu wa akatswiri okonza sitima yankhondo yapamadzi yonyamula zida zanyukiliya, msilikali wina anaganiza zosiya ntchitoyo n’kuyamba ina. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake msilikaliyu anachita zimenezi.