Zamkatimu
January 2010
Kodi Mumapanikizika ndi Ntchito?
Kodi mungatani kuti musamapanikizike kwambiri ndi ntchito?
3 Kodi Mumapanikizika ndi Ntchito?
4 Musamadzipanikize Kwambiri ndi Ntchito
7 Musamafune Zambiri Pamoyo Wanu
10 Zimene Baibulo Limanena Kodi Chidzachitike N’chiyani pa Tsiku Lachiweruzo?
16 Ulimi wa Maluwa Umafuna Khama
19 Kodi Ndi Zoona Kuti Ulamuliro wa Mfumukazi Elizabeti I Unali Wabwino?
25 Panagona Luso! Fupa Ndi Lolimba Modabwitsa
29 ‘Kuthetsa Mtima Wodzikonda’
32 Kodi Mukufuna Kukhala Bwenzi la Mulungu?
Kodi Kudyera Pamodzi Kungathandize Bwanji Banja Lanu? 13
Muziyesetsa kuti tsiku lililonse muzidyera pamodzi ndi banja lanu. Zimenezi zidzakuthandizani kukhala ndi mpata wocheza ndi banja lanu.
N’chifukwa Chiyani Anyamata Sandifunsira? 26
Kodi anyamata amafuna atsikana otani? Yankho la funsoli lingakudabwitseni kwambiri.