Zamkatimu
July 2010
Ngati Ntchito Yatha Kodi Mungasamale Bwanji Ndalama?
Ngati ntchito yakutherani, kodi mungatani kuti muzikwanitsa kukhala moyo wosalira zambiri?
3 “Pepani, Ntchito Yanu Yatha”
4 “Musade Nkhawa za Tsiku Lotsatira”
6 Kodi Mungasamale Bwanji Ndalama Zochepa Zimene Mumapeza?
14 Khoti Lina ku Spain Linagamula Kuti Mayi Wina Ali ndi Ufulu Wolera Ana Ake
15 Anyani Ochititsa Chidwi a ku Indonesia
19 Kukwera Phiri Lalitali N’koopsa Kodi Mungatani Mutadwala Pokwera Phiri?
21 Dzina la Mulungu Likulengezedwabe
23 “Mbalame Zazikulu Zouluka Mogometsa”
Kodi Ndingakwanitse Kukakhala Pandekha? 10
Nkhaniyi ikuthandizani kudziwa ngati mwakonzeka kuchoka pakhomo pa makolo anu.
“Kuphunzira Baibulo Kukuthandiza Anthu Osamva” 26
Munthu wina wolemba nkhani wa ku Czech Republic anayamikira Mboni za Yehova chifukwa chothandiza anthu osamva. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chimene chinamupangitsa kunena zimenezi.