Mawu Oyamba
Anthu ena amakayikira zoti nkhani yonena za Yesu ndi yoona, pomwe ena sakayikira n’komwe. Koma pali ena amene amanena kuti n’zosatheka kudziwa kuti zoona ndi ziti.
“Galamukani!” iyi ikufotokoza mfundo zomwe zingatithandize kudziwa zoona zake.