Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi 1 Kodi Mulungu ndi amene amachititsa kuti tizivutika? 2 Kodi mavuto athu timawachititsa tokha? 3 N’chifukwa chiyani anthu abwino amavutika? 4 Kodi tinalengedwa kuti tizivutika? 5 Kodi kuvutika kudzatha?