Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g21 No. 1 tsamba 3
  • Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala
  • Galamukani!—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
    Galamukani!—2021
  • Zimene Tingachite Kuti Tikhale Osangalala
    Nsanja ya Olonda—2010
  • Mzinda wa mu Africa Umene uli ndi Anthu a Chikhalidwe Chosiyanasiyana
    Galamukani!—2001
  • Mmene Mungapezere Chimwemwe Chenicheni
    Nsanja ya Olonda—2001
Onani Zambiri
Galamukani!—2021
g21 No. 1 tsamba 3
Mzimayi ali pamalo odyera a m’mbali mwamsewu ku India ndipo akuganizira zimene wangowerenga kumene.

Nzeru Zothandiza Kukhala Ndi Moyo Wosangalala

“Ngakhale kuti nthawi zina ndimakhumudwa ndi zinthu zoipa zimene zikuchitika m’dzikoli monga nkhondo, umphawi, matenda komanso kuchitiridwa nkhanza kwa ana, ndili ndi chiyembekezo kuti zimenezi zidzatha.”​—RANI.a

Rani anapeza chimwemwe chenicheni ataphunzira kuti Mlengi wathu, yemwe ndi Mulungu wamphamvuyonse, ndi amene amapereka nzeru zothandiza. Mukamawerenga mfundo zotsatirazi, onani mmene mfundo zomwe Mulungu akutiphunzitsa zingakuthandizireni kuti . . .

  • mukhale ndi banja losangalala

  • muzikhala mwamtendere ndi anthu ena

  • muzikhala okhutira

  • mudziwe chomwe chimachititsa kuti tizivutika komanso kufa

  • mukhale ndi chiyembekezo chabwino cha m’tsogolo

  • mumudziwe bwino Mlengi wathu komanso mukhale mnzake

Muonanso kuti Mlengi wathu samangopereka nzeru kwa anthu ochepa, koma amazipereka kwa wina aliyense amene amazifunafuna.

a Mayina asinthidwa m’magaziniyi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena