Mungapeze Buku Lina
Mbiri Yabwino Yokusangalatsani
Ife tonse timakonda mbiri yabwino, ndipo nali bukhu lathunthu lodzazidwa nayo! Bukhu lino limasimba m’kanenedwe kosabvuta chimene Baibulo limanena—m’mene iro linaperekedwera ndi mbiri yabwino imene irimo. Bukhu’lo likuchirikizidwa ndi zithunzi-thunzi zoposa makumi asanu ndi limodzi. Iro lalinganizidwa kuthandiza anthu amene akufuna kudziwa zochuluka ponena za Baibulo, ponena za m’mene linalembedwera, kumene linachokera, chimene chiri uthenga wake. Bukhu la masamba 192 Mbiri Yabwino Yokusangalatsani limachita 40c yokha, litalipiriridwatu pa positi.
Mitengo ikhoza kusintha.
Lemberani ku Watchtower, mukumagwiritsira ntchito keyala iri yonse ya pa tsamba lotsatirapo’li.