Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • jd tsamba 138
  • Yembekezerani Tsiku La Yehova Mosangalala

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yembekezerani Tsiku La Yehova Mosangalala
  • Muzikumbukira Tsiku la Yehova Nthawi Zonse
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Muziyembekezerabe’ Tsiku La Yehova
    Muzikumbukira Tsiku la Yehova Nthawi Zonse
  • “Manja Anu Asakhale Olefuka”
    Nsanja ya Olonda—1996
  • “Mundilindire”
    Nsanja ya Olonda—1996
  • Funafunani Yehova Lisanadze Tsiku la Mkwiyo Wake
    Nsanja ya Olonda—2001
Onani Zambiri
Muzikumbukira Tsiku la Yehova Nthawi Zonse
jd tsamba 138
Chithunzi patsamba 139

GAWO 4

Yembekezerani Tsiku la Yehova Mosangalala

Yehova anatumiza aneneri ake kuti achenjeze anthu za tsiku lake lamkwiyo limene likubweralo. Komabe, tisaganize kuti iye ndi Mulungu waukali. Iye ‘amafuula mosangalala chifukwa chokondwera’ ndi anthu ake. Pamene tikuyembekezera tsiku lake lalikulu, tili ndi zifukwa zomveka zotichititsa ‘kusangalala ndiponso kukondwera ndi mtima wonse.’ (Zefaniya 3:14, 17) Kodi mungatani kuti musonyeze zimenezi pa zochita zanu komanso zimene mumaganiza? Ndipo n’chifukwa chiyani muyenera kuthokoza Mulungu mukaganizira mfundo zimene mwaphunzira m’mabuku 12 a aneneri?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena