Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yp2 tsamba 172-173
  • Makolo Anu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Makolo Anu
  • Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ndingatani Kuti Ndidziwane Bwino Ndi Makolo Anga?
    Galamukani!—2009
  • Kodi Ndingatani Makolo Anga Akamakangana?
    Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
  • Kupenda Zosoŵa za Makolo Anu
    Galamukani!—1994
  • N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Samandimvetsa?
    Galamukani!—2012
Onani Zambiri
Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
yp2 tsamba 172-173

Chigawo 6

Makolo Anu

Makolo anu amadziwa zambiri. Nawonso anakhalapo ana ndipo amadziwa mavuto amene amakhalapo panthawi yaunyamata. Choncho, iwo ndi amene angakupatseni malangizo abwino omwe angakuthandizeni pamene muli wachinyamata. Komabe, nthawi zina makolo angawonjezere mavuto m’malo mokuthandizani. Mwachitsanzo, mwina mungakumane ndi mavuto ngati awa:

□ Makolo anu amangokhalira kukudzudzulani.

□ Bambo kapena mayi anu amamwa mowa mwauchidakwa kapena amagwiritsa ntchito mankhwala osokoneza bongo.

□ Makolo anu amakangana nthawi zonse.

□ Makolo anu analekana.

M’Mitu 21 mpaka 25 muona zimene mungachite mukamakumana ndi mavuto amenewa.

[Chithunzi chachikulu pamasamba 172, 173]

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena