Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 65
  • “Njira ndi Iyi”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Njira ndi Iyi”
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • “Njira Ndi Iyi”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Moyo Wopanda Mapeto—Potsiriza!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Moyo Wosatha Ulonjezedwa
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Mvetserani Mbiri ya Ufumu
    Imbirani Yehova Zitamando
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 65

Nyimbo 65

“Njira ndi Iyi”

Losindikizidwa

(Yesaya 30:20, 21)

1. Pali njira imene

Munaidziwa,

Njira yamtendere

Munaiphunzira

Pamene munamvera

Mawu a Yesu,

Ndi njira yopezeka

M’mawu a M’lungu.

(KOLASI)

Njira yakumoyo ndi ’meneyi

M’sacheuke m’sapite kumbali

Mawu a Mulungu akuti,

‘M’sapatuke njira ndi ’meneyi.’

2. Pali njira imene

Ndi yachikondi,

Tikaitsatira

Timaona kuti

Chikondi cha Mulungu

Ndi chochuluka,

Njirayi yachikondi

Imatikhudza.

(KOLASI)

Njira yakumoyo ndi ’meneyi

M’sacheuke m’sapite kumbali

Mawu a Mulungu akuti,

‘M’sapatuke njira ndi ’meneyi.’

3. Pali njira ya moyo

Imodzi yokha,

Palibe inanso

M’lungu walonjeza,

Ndi yokhayi

Tingapezemo chikondi,

Njira yakumoyotu

Ndi imeneyi.

(KOLASI)

Njira yakumoyo ndi ’meneyi

M’sacheuke m’sapite kumbali

Mawu a Mulungu akuti,

‘M’sapatuke njira ndi ’meneyi.’

(Onaninso Sal. 32:8; 139:24; Miy. 6:23.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena