Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 69
  • Ndidziwitseni Njira Zanu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndidziwitseni Njira Zanu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • Ndiphunzitseni Njira Zanu
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Muzikonda Kwambiri Choonadi Panokha
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Inuyo Panokha Muzikonda Kwambiri Choonadi
    Imbirani Yehova
  • Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 69

Nyimbo 69

Ndidziwitseni Njira Zanu

Losindikizidwa

(Salimo 25:4)

1. Yehova tasonkhanatu pamodzi

Pomvera kuitana kwanu.

Mawu anu ndi nyale m’njira yathu,

Amatiphunzitsa za inu.

(KOLASI)

Ndiphunzitseni njira zanuzo

Ndikhale womvera malamulo.

Ndiyendetseni m’njira yoona

Malamulo anu ndizikonda.

2. Nzeru zanu Yehova ndi zakuya,

Mfundo zanu n’zolimbikitsa.

Mawu anu adzakhala kosatha,

Timapezamo zodabwitsa.

(KOLASI)

Ndiphunzitseni njira zanuzo

Ndikhale womvera malamulo.

Ndiyendetseni m’njira yoona

Malamulo anu ndizikonda.

(Onaninso Eks. 33:13; Sal. 1:2; 119:27, 35, 73, 105.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena