Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ll gawo 11 tsamba 24-25
  • Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu?
  • Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
  • Nkhani Yofanana
  • Kuyandikira kwa Mulungu m’Pemphero
    Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife?
  • Tili Ndi Mwayi Wopemphera kwa Mulungu
    Zimene Baibulo Limaphunzitsa
  • Pemphero Lingakuthandizeni Kuti Mulungu Akhale Mnzanu
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Yesu Atiphunzitsa Ife Kupemphera
    Kumamumvetsera Mphunzitsi Wamkuru’yo
Onani Zambiri
Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha
ll gawo 11 tsamba 24-25

CHIGAWO 11

Kodi Yehova Amamvetsera Mapemphero Athu?

Mulungu amamva mapemphero athu. 1 Petulo 3:12

Mpando wachifumu  wa Yehova

Yehova ndi “Wakumva pemphero.” (Salimo 65:2) Iye amafuna kuti tizimuuza zakukhosi kwathu.

Munthu akupemphera

Muzipemphera kwa Yehova yekha osati kwa wina aliyense.

  • Yesu anatiphunzitsa mmene tingapempherere.—Mateyu 6:9-15.

  • Kodi Mulungu amamvetsera mapemphero a ndani?​—Salimo 145:18, 19.

Pali zinthu zambiri zimene tingatchule popemphera. 1 Yohane 5:14

Yesu ndi a 144,000 mu Ufumu wake

Muzipemphera kuti chifuniro cha Mulungu chichitike kumwamba komanso padziko lapansi pano.

Muzipemphera m’dzina la Yesu, kuti musonyeze kuti mumayamikira zimene iye anakuchitirani.

Mkhristu amene amadalira Yehova kuti amuthandize komanso amathandiza banja lake ndipo amachita zabwino

Pemphani Yehova kuti akuthandizeni kuchita zinthu zabwino. Mungapemphe zinthu monga chakudya, ntchito, nyumba, zovala ndiponso thanzi labwino.

  • Yehova amamva mapemphero a anthu amene amachita zolungama.​—Miyambo 15:29.

  • Musamade nkhawa.​—Afilipi 4:6, 7.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena