Kodi Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambiri Okhudza Moyo?
Kodi mayankhowo tingawapeze . . .
kwa asayansi?
kwa anthu anzeru?
m’Baibulo?
WOLEMBA BAIBULO WINA ANAPEMPHA MULUNGU KUTI,
“Ndithandizeni kukhala wozindikira . . . Mawu anu onse ndi choonadi.”—Salimo 119:144, 160, Baibulo la Dziko Latsopano.
Baibulo likuyankha mafunso a anthu ambiri.
Kodi mungakonde kukhala ena mwa anthu amenewo?
Webusaiti ya jw.org ingakuthandizeni kuyankha mafunso anu.
WERENGANI zimene zili pa intaneti
Werengani Baibulo m’zinenero zoposa 100
Mayankho a mafunso a m’Baibulo
Nkhani zothandiza mabanja
ONERANI mavidiyo a nkhani za m’Baibulo
Okhudza nkhani ndiponso nyimbo zophunzitsa ana
Okhudza malangizo othandiza achinyamata
Okhudza mmene anthu a Yehova anasonyezera chikhulupiriro
PANGANI DAWUNILODI mabuku
Kabuku kakuti, Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale
Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani!
PA MAFUNSO OMWE ALI M’MUNSIWA, KODI NDI FUNSO LITI LOMWE MUMAFUNA MUTADZIWA YANKHO LAKE?
Kodi cholinga cha moyo n’chiyani?
Kodi Mulungu ndi amene amachititsa kuti tizivutika?
Kodi chimachitika n’chiyani munthu akamwalira?
Pezani mayankho ochokera m’Baibulo a mafunso amenewa pa webusaiti ya jw.org.
(Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)