Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
MUTU
Akufa adzaukitsidwa 48, 86, 91, 93
Ana inu, muzitumikira Yehova 37, 51, 59, 61, 72, 100
Kudzikonda kungachititse kuti ifeyo komanso anthu ena akumane ndi mavuto 3, 4, 12, 27, 28, 39, 49, 88
Kulambira konyenga kumachokera kwa Mdyerekezi 19, 20, 22, 38, 46, 49, 52, 58
Mkwiyo ndi woopsa 4, 12, 41, 45, 49, 65, 89
Muzikwaniritsa zimene mwalonjeza ngati mmene amachitira Yehova 8, 9, 11, 23, 24, 31, 34, 35, 36, 66, 93
Mulungu amadana ndi anthu oukira 7, 17, 26, 27, 28, 88
Musamachite zoipa 14, 27, 49, 53, 58, 88, 89
Musamataye mtima mukakumana ndi mavuto 16, 47, 51, 57, 64, 75, 90, 95, 99, 101
Musataye zimene Yehova wakupatsani 12, 13, 24, 35, 36, 56, 75, 95, 100
Muzikhululuka ngati Yehova 13, 15, 31, 43, 92
Muzimvera kuti mukhale ndi moyo 3, 5, 10, 37, 39, 54, 59, 65, 72
Muziyamika Yehova nthawi zonse 2, 6, 67, 103
N’zosatheka kukonda Mulungu ngati simukonda anzanu 4, 13, 15, 41
Oipa onse sadzakhalakonso 5, 10, 32, 46, 102
Simungatumikire Mulungu ndi chuma nthawi imodzi 10, 17, 44, 59, 75, 76
Tizigwirizana ndi anthu amene amakonda Yehova 16, 33, 42, 80, 87, 100, 103
Tizilalikira uthenga wabwino wa Ufumu 73, 76, 94, 95, 96, 97, 98
Tizimvera Yesu chifukwa ndi Mfumu ya Ufumu wa Mulungu 74, 78, 79, 83, 84, 85, 91, 92, 99
Ufumu wa Mulungu udzapangitsa kuti aliyense azikhala mosangalala 1, 48, 62, 79, 81, 83, 85, 86
Yehova adzatithandiza choncho tizichita zinthu molimba mtima 40, 47, 51, 53, 57, 61, 64, 65, 76, 88, 101
Yehova akhale mnzanu 11, 30, 33, 51, 56, 59, 69, 81, 82
Yehova amakonda anthu a mitundu yonse 30, 33, 48, 54, 77, 94, 97, 98, 99
Yehova amamvetsera tikamapemphera kuchokera mumtima 35, 38, 50, 64, 82
Yehova amaona kuti anthu onse ndi amtengo wapatali 8, 9, 11, 21, 23, 68, 70, 74, 87, 90
Yehova amateteza anthu amene amamukonda 6, 22, 40, 50, 52, 55, 64, 71, 84
Yehova amateteza anthu odzichepetsa 43, 45, 65, 67, 69
Yehova amatsogolera anthu ake 18, 25, 26, 27, 29, 34, 39, 44, 73, 80
Yehova analenga dziko kuti tizikhalamo 1, 2, 102, 103
Yehova anatipatsa Baibulo kuti litithandize kupeza nzeru 56, 66, 72, 75, 81
Yehova ndi Wamphamvuyonse 1, 7, 18, 19, 20, 21, 22, 26, 55, 60
Yehova saiwala zimene tamuchitira 16, 29, 32, 48, 65, 69, 77, 100
Yehova sanama 3, 10, 16, 63, 68, 70, 102, 103
Zimene Mulungu amafuna zidzachitika padzikoli ngati mmene zilili kumwamba 25, 55, 60, 62, 63, 71, 96, 102